ENVIAR LETRAS
Top 100
Lançamentos de álbuns
Artistas
Comunidade
francês
Espanhol
Português
corrija a letra Letra
BWANJI/KUSELI
por
Teddy
Retornar
Letra
Ndikudziwa timacheza Ndikudziwa unandiuza Mtima wako unasweka Pano chikondi suchifuna Koma nanga ndipange bwanji Tandiuze ndipange bwanji Nthawi yonseyi Ndinkayesa ukhala chabe friend Ndadziwa pano ndinapanga mistake Ndili ndi mantha kodi sukhumudwa iwe Ndikakuuza ndimakufuna Ndikakuuza ndimakufuna Koma nanga ine ndipange bwanji Tandiuze ine ndipange bwanji Ooh I fell in love ndipo si za jokes Mami ine ndipange bwanji Kuseli, kuseli Ndimaka dumpha dumpha ndikakuona Chikondwelelo chake cha mpeni (uh) Mami ukandigunda thupi langa limagwidwa nyesi (uh) Ndipo ukandi caller phone singalile kawili yeah Nthawi yonseyi Ndinkayesa ukhala chabe friend Ndadziwa pano ndinapanga mistake Ndili ndi mantha kodi sukhumudwa iwe Ndikakuuza ndimakufuna Ndikakuuza ndimakufuna Koma nanga ine ndipange bwanji Tandiuze ine ndipange bwanji Ooh I fell in love ndipo si za jokes Mami ine ndipange bwanji Please don't call me your brother ndikawulula Zonse za ku mtima kwanga ndikakhuthula Chonde usandikwiyile nkundituluka Ndayesesa kupilila osakuuza Chabe mami ndimakukonda Baby ine ndimakukonda Ndimakukonda konda
vídeo de música
Seu nome será publicado. Deixe os campos em branco para permanecer anônimo.
Enviar
Modal title
×
Adicionar mídia
Video URL?
(YouTube, Vimeo, Instagram, DailyMotion, Soundcloud)
×
Lembre de mim
Senha perdida
Entrar
Registrarse