AJOUTER PAROLES
Top 100
Sorties d'albums
artistes
Communauté
Espagnol
Portuguais
Anglais
Correction Paroles
DESPERATE
par
Teddy
Retour
Paroles
M’ma Makadidido eeh Oh yeah, oh yeah, ooh yeah I know it’s not okay Kuti nthawi zonse nzikukulonda iwe Baby I can’t help it I still belive the odds will play in my favour Do you think of me Olo mwina zoyi ndakusowa iweyo Nthawi yonseyi Ndinkaganiza zoti sungagwidwe Kapena mwina m’minyama (aaah) Zoti unandithawa (aah) Pano yatsala ndi nkhawa (aah) Iwe sunkandikonda (aah) Kodi unandinamiza? (aah) When you told me love always wins Ine ndimanva kuwawa Daily nkama ku stalker (and) I know it’s not okay It’s not okay It’s not okay It’s not okay Baby I am desperate I am desperate I am desperate I am desperate Ma ine, ma ine Daily m’mangoganiza za iwe Anzanga nawo amathoka za iwe Anzako nawo akuti you’re happy iwe Nnaziyambilanji za chikondi izi? Zanga zimangothela misonzi Why do you look better and excited? Zaka zonsezi sunawonekepo chonchi iwe Kapena mwina m’minyama (aaah) Zoti unandithawa (aah) Pano yatsala ndi nkhawa (aah) Iwe sunkandikonda (aah) Kodi unandinamiza? (aah) When you told me love always wins Ine ndimanva kuwawa Daily nkama ku stalker (and) I know it’s not okay It’s not okay It’s not okay It’s not okay Baby I am desperate I am desperate I am desperate I am desperate Kapena mwina m’minyama (aaah) Zoti unandithawa (aah) Pano yatsala ndi nkhawa (aah) Iwe sunkandikonda (aah) Kodi unandinamiza? (aah) When you told me love always wins Ine ndimanva kuwawa Daily nkama ku stalker (and)
clip
Ton pseudo sera publié. Laisses les champs vide pour rester anonyme.
Soumettre
Modal title
×
Ajouter un média
Video URL?
(YouTube, Vimeo, Instagram, DailyMotion, Soundcloud)
×
Se souvenir de moi
Mot passe oublié
Connectes-toi
M'inscrire