ENVIAR LETRAS
Top 100
Lanzamientos de álbumes
Artistas
Comunidade
Francés
Portuguese
Inglés
Corrección Letra
Mtopola
par
M.anifest
Regreso
Letra
Ah Hee Ah Hee Ah Hee Yeah hee Mukukamba zinkhani zambiri Mukafuna ndiwononge mbiri Kodi nchikondi Ndimayesa tilimo awiri Muli ndi nthawi muli busy Chonde msachimwise Ayi nsadanise Ndi wangayu Achuluka anthu okhomelela ahahaha Kankhani pang'ono kukhomelela koma why ATI ndingofuna ndingokudyela ineyo Atumapo anthu kuzandikwenya ndee Tinamenyana Mumvetse Olo mu dameje dameje Kumuleka sizingatheke Ndimadana ndi mtopola Muleke Zomakamuwuza miseche Ndicholinga choti athese Ndimadana ndi mtopola Ine ndimadana ndi mtopola Mtopola eh mtopola Mtopola eh mtopola Ndimadana ndi mtopola Ndati ndimadana ndi mtopola Mtopola eh mtopola Mtopola eh mtopola Ndimadana ndi mtopola Yeah Umaganiza bwanji kukwatira beast Iweyo ndi Ka beauty ofunika Prince Mamuna Oti nthumba anathila yeast Osati kafinyanya wonunkha gilisi Mhuu koma mtopola Ndizamumveso wina nzamunokola Kumawuza anzake andisomphola Ndizamponda pamutu ndi chigogoda Cell nzalowa Bola ndamtchola Eya pezani zina zochita Eya kupeza wanu nzovuta Eya mungomupempha Chauta Osativuta Mwachuluka anthu okhomelela Kankhani pang'ono kupemelela ATI ndingofuna ndingokudyela Koma tizamenyana Mumvetse Olo mu dameje dameje Kumuleka sizingatheke Ndimadana ndi mtopola Muleke Zomakamuwuza miseche Ndicholinga choti athese Ndimadana ndi mtopola Ine ndimadana ndi mtopola Mtopola eh mtopola Mtopola eh mtopola Ndimadana ndi mtopola Ndati ndimadana ndi mtopola Mtopola eh mtopola Mtopola eh mtopola Ndimadana ndi mtopola Olo mu dameje dameje Kumuleka sizingatheke Olo mumuwuze miseche Yeah ey yeah Yeah ey yeah Ndimadana ndi mtopola Mtopola eh mtopola Mtopola eh mtopola Ndimadana ndi mtopola Ndati ndimadana ndi mtopola Mtopola eh mtopola Mtopola eh mtopola Ndimadana ndi mtopola Mtopola eh mtopola Mtopola eh mtopola Ndimadana ndi mtopola Mtopola eh mtopola Mtopola eh mtopola Ndimadana ndi mtopola
videoclip
Tu nombre será publicado. Deje los campos en blanco para permanecer en el anonimato.
Enviar
Modal title
×
Insertar medios
Video URL?
(YouTube, Vimeo, Instagram, DailyMotion, Soundcloud)
×
Recuérdame
Contraseña perdida
Conectarte
Registrarse